Song Artwork

Saint ft Skeffa Chimoto – Uzindipephelera Song Lyrics

Artists: Saint ft Skeffa Chimoto

Tittle: Uzindipephelera

Produced by: OBK and Sispence

Released on: 23 March 2020

(Saint)

Oooh ooh oooooh

Mmmmh, darle wangu

Mkazi wanga. Eehe yeah.

Verse 1: {Saint}

Tokoma sititi leke, darle

Kukukonda sindingaleke eh

Darle yeah

Koma zonsezi kuti zitheke

Mpaka kale eeeh eeh yeah

Tisamangoti I love you,

I love you

Tu…yenera kukomza tsogolo lathu

Nowadays timaubwenzi tukhala ta temporary

Amayamba ndi moto after 2 days chikondi chapola kale

Kubzala mbeu ya Chikondi pa mwala, mawa yafota kale

Yahweh akakhala wotsogolera

Dziwa kutali konse tikafikila So…

Chorus:

Zindipemphelerabe nane Mzikupemphelerabe

Zindipemphelerabe,izi zimkele, zimkelebe

Pemphelerabe…

Nane, Mzikupemphelerabe

Zindipemphelerabe Ambuye adalitse

Dalitse Ambuye.

Bridge:

So pray for me,

Pray for me my love

And I will keep praying for you

Praying for you my love.

Hey Skeffa

Verse 2 {Skeffa Chimoto}

Nkhani zomwe zimandipeza

Zomwe umayankhula ndi amzako

Ndimamva kuti umandiyamikila

Kuti ndine Mbambande eeh

Ukuti ndine wooneka bwino

Ukuti ndine olimbika ntchito

Ukutiso ndimatha kusamala banja

Ndipo ndimakwanira

Koma chimodzi ndifuna ndikupemphe

Chonde udzipezako nthawi

Kugwada pansi

Pamaso pa Mbuye kumandipemphelera

Akapanda kumanga banja

Yahweh Chisumphi Namalenga

Udziwe wolimangayo alimanga chabe eeeh

Chorus: x2

Zindipemphelerabe,

{Pemphelerabe}

Nane Mzikupemphelerabe {Pemphelerabe}

Zindipemphelerabe,izi zimkele, zimkelebe

{pemphelera kuti dzimkele dzimkele dzimkele}

Pemphelerabe {pemphelerabe}

Nane Mzikupemphelerabe {Pemphelerabe}

Zindipemphelerabe Ambuye adalitse

Dalitse Ambuye.

{Adalitse adalitse adalitse}

Bridge {Skeffa Chimoto}

So pray for me

Pray for me my love

I will be praying for you my love

Yeaah

Pray for me my love

I will keep praying for you every-time baby

Comments

comments

About Entertainment Malawi

Leave a Reply

x

Check Also

Download “Pa Ntondo” by Phyzix (Prod. Janta).mp3

Click the file (song title) to Download # File Description File size 1 Pa Ntondo ...